1 Mafumu 14:8 BL92

8 ndipo ndinalanda nyumba ya Davide ufumu, ndi kuupereka kwa iwe, koma sunafanana ndi Davide mtumiki wanga uja, amene anasunga malamulo anga, nanditsata ndi mtima wace wonse kucita zolunjika zokha zokha pamaso panga;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:8 nkhani