1 Mafumu 15:19 BL92

19 Pakhale pangano pakati pa ine ndi inu, pakati pa atate wanga ndi atate wanu; taonani, ndatumiza kwa inu mphatso ya siliva ndi golidi, tiyeni lilekeke pangano liri pakati pa inu ndi Basa mfumu ya Israyeli, kuti andicokere.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 15

Onani 1 Mafumu 15:19 nkhani