1 Mafumu 15:24 BL92

24 Nagona Asa ndi makolo ace, naikidwa kwa makolo ace m'mudzi wa Davide kholo lace; ndipo Yosafati mwana wace analowa ufumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 15

Onani 1 Mafumu 15:24 nkhani