1 Mafumu 15:5 BL92

5 cifukwa kuti Davide adacita colungama pamaso pa Yehova, osapambuka masiku ace onse pa zinthu zonse adamlamulira iye, koma cokhaco cija ca Uriya Mhiti.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 15

Onani 1 Mafumu 15:5 nkhani