1 Mafumu 16:29 BL92

29 Ndipo caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi zitatu ca Asa mfumu ya Yuda Ahabu mwana wa Omri analowa ufumu wa Israyeli, nakhala Ahabu mwana wa Omri mfumu ya Israyeli m'Samaria zaka makumi awiri mphambu ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 16

Onani 1 Mafumu 16:29 nkhani