1 Mafumu 17:23 BL92

23 Ndipo Eliya ananyamula mwanayo, natsika naye ku cipinda cosanja, nalowa naye m'nyumba, nampereka kwa amace; nati Eliya, Taona, mwana wako ali moyo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:23 nkhani