1 Mafumu 18:13 BL92

13 Kodi sanakuuzani mbuye wanga cimene ndidacita m'kuwapha Yezebeli aneneri a Yehova, kuti ine ndidabisa aneneri a Yehova zana limodzi makumi asanu asanu m'phanga, ndikuwadyetsa mkate ndi madzi?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:13 nkhani