1 Mafumu 18:19 BL92

19 Ndipo tsono, tumani mundimemezere Aisrayeli onse ku phiri la Karimeli, ndi aneneri a Baala mazana anai mphambu makumi asanu, ndi aneneri a cifanizoco mazana anai, akudya pa gome la Yezebeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:19 nkhani