1 Mafumu 18:27 BL92

27 Ndipo pausana Eliya anawaseka, nati, Kwezani mau, popeza ndiye mulungu; kapena alikulingirira, kapena wapambuka, kapena ali paulendo, kaya agona, adzagalamuka.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:27 nkhani