29 Ndipo kunali, litapendeka dzuwa, ananenera kufikira nthawi ya kupereka nsembe; koma panalibe mau, kapena wobvomereza, kapena wakuwamvera.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18
Onani 1 Mafumu 18:29 nkhani