31 Ndipo Eliya anatenga miyala khumi ndi iwiri, monga mwa ciwerengo ca mafuko a ana a Yakobo, amene mau a Yehova adamfikira, kuti, Dzina lako ndi Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18
Onani 1 Mafumu 18:31 nkhani