1 Mafumu 18:4 BL92

4 pakuti pamene Yezebeli anapulula aneneri a Yehova, Obadiya anatenga aneneri zana limodzi, nawabisa makumi asanu asanu m'phanga, nawadyetsa mkate ndi madzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:4 nkhani