1 Mafumu 19:3 BL92

3 Ndipo iye ataona cimeneci, ananyamuka, nathawa kupulumutsa moyo, nafika ku Beereseba wa ku Yuda, nasiya mnyamata wace pamenepo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 19

Onani 1 Mafumu 19:3 nkhani