1 Mafumu 19:8 BL92

8 Tsono anauka, nadya namwa, nayenda ndi mphamvuya cakudya cimeneco masiku makumi anai usana ndi usiku, nafika ku phiri la Mulungu ku Horebu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 19

Onani 1 Mafumu 19:8 nkhani