1 Mafumu 2:13 BL92

13 Pomwepo Adoniya mwana wa Hagati anadza kwa Batiseba amai wace wa Solomo, ndipo mkaziyo anati, Kodi wadza ndi mtendere? Nati, Ndi mtendere umene.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:13 nkhani