31 Ndipo mfumu inati kwa iye, Cita monga umo wanena iye, numkwere, numuike; kuti undicotsere ine ndi nyumba ya atate wanga mwazi uja Yoabu anaukhetsa wopanda cifukwa.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2
Onani 1 Mafumu 2:31 nkhani