1 Mafumu 2:33 BL92

33 Motero mwazi wao udzabweranso pa mutu wace wa Yoabu, ndi pa mutu wa mbumba yace, ku nthawi yamuyaya; koma Davide, ndi mbumba yace, ndi banja lace, ndi mpando wace wacifumu adzakhala ndi mtendere wa Yehova ku nthawi yamuyaya.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:33 nkhani