38 Ndipo Simeyi ananena ndi mfumu, Mau awa ndi abwino; monga momwe mwanena mbuye wanga mfumu momwemo ndidzacita kapolo wanu. Ndipo Simeyi anakhala m'Yerusalemu masiku ambiri.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2
Onani 1 Mafumu 2:38 nkhani