1 Mafumu 2:4 BL92

4 kuti Yehova akakhazikitse mau ace adanenawo za ine, kuti, Ngati ana ako akasunga bwino njira zao, kuyenda moona pamaso pa Ine ndi mtima wao wonse ndi moyo wao wonse, nditi sipadzakusowa mwamuna mmodzi pa mpando wacifumu wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:4 nkhani