1 Mafumu 2:46 BL92

46 Pamenepo mfumu inalamulira Benaya mwana wa Yehoyada, ndipo iye anaturuka namkwera, namwalira iye. Ndipo ufumu unakhazikika m'dzanja la Solomo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 2

Onani 1 Mafumu 2:46 nkhani