1 Mafumu 20:29 BL92

29 Ndipo awa anakhala m'misasa pandunji pa ajawo masiku asanu ndi awiri. Tsono kunali, tsiku lacisanu ndi ciwiri anayambana nkhondo; ndipo ana a Israyeli anaphako Aaramu tsiku limodzi anthu oyenda pansi zikwi zana limodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:29 nkhani