1 Mafumu 20:38 BL92

38 Pamenepo mneneriyo anamuka, nadikira mfumu pamseu, nadzizimbaitsa ndi mpango pamaso pace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:38 nkhani