4 Ndipo mfumu ya Israyeli anayankha, nati, Monga mwanena, mbuye wanga mfumu, ndine wanu ndi zonse ndiri nazo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20
Onani 1 Mafumu 20:4 nkhani