14 Pomwepo anatuma mau kwa Yezebeli, nati, Naboti waponyedwa miyala, nafa.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21
Onani 1 Mafumu 21:14 nkhani