1 Mafumu 21:22 BL92

22 ndipo ndidzalinganiza nyumba yako ndi nyumba ya Yerobiamu mwana wa Nebati, ndi ya Basa mwana wa Ahiya; cifukwa ca kuputa kumene unaputa nako mkwiyo wanga, ndi kucimwitsa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:22 nkhani