1 Mafumu 21:27 BL92

27 Ndipo kunali, pakumva Ahabu mau amenewa, anang'amba zobvala zace, nabvala ciguduli pathupi pace, nasala kudya, nagona paciguduli, nayenda nyang'anyang'a.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 21

Onani 1 Mafumu 21:27 nkhani