1 Mafumu 22:15 BL92

15 Ndipo atafika kwa mfumu, mfumu inati kwa iye, Mikaya, kodi tizimuka ku Ramoti Gileadi kukathira nkhondo, kapena tileke? Nati iye, Kwerani, ndipo mudzacita mwai, popeza Yehova adzaupereka m'dzanja la mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:15 nkhani