17 Nati iye, Ndinaona Aisrayeli onse obalalika pamapiri ngati nkhosa zopanda mbusa; ndipo Yehova anati, Izi ziribe mwini, yense abwerere ndi mtendere ku nyumba yace.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:17 nkhani