1 Mafumu 22:22 BL92

22 Nati, Ndidzaturuka, ndidzakhala mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri ace onse. Nati, Udzamnyengadi, nudzakhozanso; turuka, ukatero kumene.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:22 nkhani