24 Pamenepo Zedekiya mwana wa Kenana anasendera, napanda Mikaya patsaya, nati, Mzimu wa Yehova wandicokera bwanji, kulankhula ndi iwe?
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:24 nkhani