1 Mafumu 22:28 BL92

28 Ndipo Mikaya anati, Mukabwera ndithu ndi mtendere Yehova sanalankhula mwa ine. Nati, Mvetsani, anthu inu nonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:28 nkhani