3 Ndipo mfumu ya Israyeli ananena ndi anyamata ace, nati, Kodi simudziwa kuti Ramoti Gileadi ngwathu, ndipo tangokhala cete, osaulanditsa m'dzanja la mfumu ya Aramu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:3 nkhani