1 Mafumu 22:41 BL92

41 Koma Yehosafati mwana wa Asa anayamba kukhala mfumu ya Yuda caka cacinai ca Ahabu mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22

Onani 1 Mafumu 22:41 nkhani