43 Ndipo anayenda m'njira yonse ya atate wace Asa, osapambukamo; nacita coyenera pamaso pa Yehova, koma misanje sanaicotsa; anthu anapherabe nsembe, nafukiza zonunkhira pamsanje.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 22
Onani 1 Mafumu 22:43 nkhani