1 Mafumu 3:13 BL92

13 Ndiponso zimene sunazipempha adakupatsa, ndipo cuma ndi ulemu, kuti pakati pa mafumu sipadzakhala yina yolingana ndi iwe masiku ako onse.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:13 nkhani