1 Mafumu 3:17 BL92

17 Ndipo mkazi mmodzi anati, Mbuye wanga, ine ndi mkazi uyu tikhala awiri m'nyumba imodzi; ndipo ine ndinaona mwana, iye ali m'nyumbamo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:17 nkhani