1 Mafumu 3:26 BL92

26 Koma mkazi amene mwana wamoyo anali wace analankhula ndi mfumu, popeza mtima wace unalira mwana wace, nati, Ha! mbuye wanga, mumpatse uyo mwana wamoyo osamupha konse. Koma winayo anati, Asakhale wanga kapena wako, dulani.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:26 nkhani