1 Mafumu 3:28 BL92

28 Ndipo Aisrayeli onse anamva maweruzidwe ace idaweruza mfumu, naopa mfumu; pokhala anaona kuti nzeru ya Mulungu inali mwa iye yakuweruza.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 3

Onani 1 Mafumu 3:28 nkhani