1 Mafumu 4:13 BL92

13 Benigeheri ku Ramoti Gileadi, iyeyo anali nayo midzi ya Yairo mwana wa Manase iri m'Gileadiyo, iye anali nalo dziko la Arigobi liri m'Basani, midzi yaikuru makumi asanu ndi limodzi yamalinga ndi zitseko zamkuwa;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 4

Onani 1 Mafumu 4:13 nkhani