1 Ndipo Hiramu mfumu ya ku Turo anatuma anyamata ace kwa Solomo, popeza anamva kuti adamdzoza mfumu m'malo mwa atate wace; pakuti Hiramu adakondana ndi Davide masiku onse.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5
Onani 1 Mafumu 5:1 nkhani