1 Mafumu 5:11 BL92

11 Ndipo Solomo anapatsa Hiramu miyeso ya tirigu zikwi makumi awiri ndiyo zakudya za banja lace, ndi miyeso makumi awiri ya mafuta oyera; motero Solomo anapatsa Hiramu caka ndi caka.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 5

Onani 1 Mafumu 5:11 nkhani