10 Ndipo anamanga zipindazo zogundana ndi nyumba yonseyo, cipinda ciri conse msinkhu wace mikono isanu; ndipo anazilumikizitsa kunyumba ndi mitengo yamkungudza.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6
Onani 1 Mafumu 6:10 nkhani