1 Mafumu 6:15 BL92

15 Ndipo anacinga makoma a nyumba m'katimo ndi matabwa amkungudza, kuyambira pansi kufikira posanja, nacinga m'katimo ndi matabwa, nayala pansi m'nyumbamo matabwa amlombwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:15 nkhani