1 Mafumu 6:18 BL92

18 Ndipo m'kati mwa nyumba munali mikungudza yosemasema, ngati zikho ndi maluwa oti gada; munali mikungudza yokha yokha simunaoneka mwala ai,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:18 nkhani