1 Mafumu 6:21 BL92

21 Momwemo Solomo anakuta m'kati mwa nyumba ndi golidi woyengetsa, natambalika maunyolo agolidi cakuno ca monenera, namukuta ndi golidi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:21 nkhani