1 Mafumu 6:36 BL92

36 Ndipo bwalo la m'kati analimanga mizere itatu ya miyala yosemasema, ndi mzere umodzi wa mitanda yamkungudza.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 6

Onani 1 Mafumu 6:36 nkhani