1 Mafumu 7:12 BL92

12 Ndipo bwalo lalikuru lozingapo linali ndi mizere itatu ya miyala yosemasema, ndi mzere umodzi wa mitanda yamkungundza, monga bwalo la pakati pa nyumba ya Yehova, ndi likole la nyumbayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:12 nkhani