15 Popeza iyeyu anaunda nsanamira ziwiri zamkuwa, msinkhu wace wa imodzi unali mikono khumi mphambu isanu ndi itatu; ndipo cingwe ca mikono khumi mphambu iwiri cinayesa thupi la nsanamira imodzi.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7
Onani 1 Mafumu 7:15 nkhani