1 Mafumu 7:17 BL92

17 Ndipo panali maukonde olukaluka ndi zoyangayanga, zokolana za pa mitu imene inali pamwamba pa nsanamira; zisanu ndi ziwiri za pa mutu wina, ndi zisanu ndi ziwiri za pa mutu unzace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:17 nkhani