1 Mafumu 7:30 BL92

30 Ndipo phaka lid lonse linali ndi njinga zamkuwa zinai ndi mitanda yamkuwa, ndipo ngondya zace zinai zinali ndi mapewa; pansi pa thawale panali mapewa oyengeka pa mbali pa zophatikizika zonse.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:30 nkhani